Pamene Aisraele anamasulidwa ku ukapolo ku Igipito, pamene analowa m ‘dziko lolonjezedwa la Kanani, pamene Mfumu Yosiya ndi Mfumu Hezekiya, amene ankalambira mafano, anabwerera kwa Mulungu, ndipo ngakhale pamene Aisraele anamasulidwa ku ukapolo, Paska anali gwero.
Mofanana ndi nthawi imeneyo, ntchito ya Mulungu yopulumutsa ikuchitika kudzera mu Paska lero.
Zaka thusauzande zapitazo, Paska wa pangano latsopano, amene Yesu anafunitsitsa kusunga ndi ophunzira Ake, anachotsedwa mu AD 325 chifukwa cha mgwirizano pakati pa chipembedzo ndi ndale ndipo anasowa mu nthawi ya mdima; Komabe, monga analosera, Khristu Ahnsahnghong anabwera ndi kuyamba ntchito ya chipulumutso kudzera Paska.
“Ndipo anati kwa iwo, “Ndinalakalaka
ndithu kudya Paska uwu pamodzi
ndinu, ndisanayambe kusautsidwa.”
Luka 22:15
“Ndipo tsiku loyamba la Mkate Wopanda
Chotupitsa, ophunzira anadza kwa Yesu, nati,
Mufuna tikakonzere kuti Paska, kuti mukadye?”
Nati Iye, “Mukani kumzinda kwa munthu
wina wake, mukati kwa Iye, ‘Mphunzitsi anena,
Nthawi yanga yayandikira; ndidzadya Paska
kwanu pamodzi ndi ophunzira anga.’”
Mateyu 26:17–18
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi