Baibulo limaneneratu kuti Yerusalemu wapadziko lapansi unakhazikitsidwa ndi Mulungu ngati mthunzi kuti atisonyeze zenizeni, Yerusalemu wauzimu, Amayi Akumwamba.
Chifukwa chake, kumbuyo kwa tanthauzo lomwe anthu ambiri amaika paulendo wopita ku Yerusalemu ndi tanthauzo loti tiyenera kubwera ku Yerusalemu, Mulungu Amayi.
Aneneri ambiri ananeneratu kuti chipulumutso chimabwera tikabwelera kwa Yerusalemu Amayi, ndipo Khristu Ahnsahnghong ananenanso, “Ndimatsatira Amayi.”
Choncho, ngati mwawerenga ndi kumva mawu awa, muyenera kubwera kwa Mulungu Amayi malinga ndi ziphunzitso izi ndi kudalitsidwa ndi Mulungu.
Koma Yerusalemu wa kumwamba uli waufulu, ndiwo amai wathu.
Agalatiya 4:26
Ndipo Mzimu ndi mkwatibwi anena, Idzani. Ndipo wakumva anene, Idzani. Ndipo wakumva ludzu adze; iye wofuna, atenge madzi a moyo kwaulere.
Chivumbulutso 22:17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi