Mtumwi Yohane analosera kuti Mzimu
ndi Mkwatibwi yekha ndi amene
angapatse anthu madzi a moyo.
Tikhoza kudziwa kuti Mzimu ndi
Mkwatibwi ndi ndani pofufuza mau a m’Baibulo;
Mulungu adalenga mwamuna ndi mkazi
m’chifanizo cha Mulungu ndipo Yerusalemu
wakumwamba ndi Amayi wathu monga
kwalembedwa buku la Agalatiya.
Iwo ndi Atate Khristu Ahnsahnghong,
amene anabwera ngati Mzimu,
ndi Mulungu Amayi.
Gulu la Utumiki wa Dziko
Lonse Mpingo wa Mulungu ndi
kumene Mulungu Atate ndi Mulungu
Amayi amaitanira anthu kuti abwere
kudzalandira chikhululukiro cha machimo, moyo
wosatha, ndi chipulumutso.
Chifukwa chimene mpingo umagwiritsira ntchito
mayina audindo “Atate”, “Amayi”, “M’bale”
ndi “Mlongo” n’chakuti anthu onse
ali m’banja lakumwamba.
Mulungu ndiye Atate wathu ndi Amayi athu.
Ndipo Mzimu ndi mkwatibwi anena,
Idzani. Ndipo wakumva anene, Idzani.
Ndipo wakumva ludzu adze; iye
wofuna, atenge madzi a moyo kwaulere.
Chivumbulutso 22:17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi