Phwando la Mkate Wopanda Chotupitsa
ndi phwando pamene Yesu Khristu
ananyamula mtanda wozunzika
chifukwa cha ochimwa.
Mulungu amatiphunzitsa kuti pamene anthu
onse, ochimwa akumwamba, atsatira chitsanzo cha
Khristu, kunyamula mtanda wawo, ndi kutsatira
njira ya Khristu, akhoza kukhala ndi chikhumbo
cha umuyaya kupyolera m’masautso ndi zowawa.
Oyera mtima a Mpingo woyamba anazindikira
kuti pali moyo wosatha utatha moyo padziko
lapansi pano ndipo anavomereza mokondwera
masautso onse, zowawa, ndi mazunzo
ndi chikhumbo cha muyaya.
Momwemonso, mamembala a mpingo
wa Mulungu nthawi zonse
amayamika pa chilichonse chomwe
amakumana nacho padziko lapansi.
Ndaona vuto limene Mulungu
wapatsa ana a anthu kuti avutidwe nalo.
Chinthu chilichonse anachikongoletsa
pa mphindi yake; ndipo waika
zamuyaya m'mitima yao . . .
Mlaliki 3:10-11
Chifukwa chake sitifooka; . . .
Pakuti chisautso chathu chopepuka
cha kanthawi chitichitira ife kulemera
koposa kwakukulu ndi kosatha kwa ulemerero;
2 Akorinto 4:16-17
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi