M’banja la Abulahamu,
Eliezere ndi Isimaeli sanalandire
cholowa.
Isake, yemwe anali wamng’ono
pa onse, analandira cholowa
kudzera mwa bambo ndi
mayi ake amene
anali mfulu.
Ili ndi phunziro limene Mulungu akuphunzitsa anthu.
Ngakhale lero, tikakhala ana
a Atate Ahnsahnghong ndi
Mulungu Amayi kudzera
mu pangano latsopano,
titha kukhala ansembe achifumu
kumwamba monga olowa
nyumba a Mulungu.
Pamene Yesu ananena kuti,
“Iwe ulibe gawo ndi
Ine,” Petro anadabwa kwambiri
chifukwa ndi okhawo amene
ali ndi mbali ndi
Mulungu amene angalowe
mu ufumu wakumwamba.
Ichi ndi chifukwa chake
mamembala a Mpingo wa
Mulungu amalalikira za
Mulungu Atate ndi Mulungu
Amayi ku dziko lonse
lapansi ndi kuwaunikira kuti
ubale wapakati pa Mulungu
ndi anthu ndi ubale
wa Makolo ndi ana.
Koma Yerusalemu wa kumwamba
uli waufulu, ndiwo
amai wathu.
Agalatiya 4:26
ndipo ndidzakhala kwa
inu Atate, ndi inu
mudzakhala kwa Ine ana
aamuna ndi aakazi,
anena Ambuye Wamphamvuyonse.
2 Akorinto 6:18
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi