Ngakhale kuti mtumwi Paulo anatsekera m’ndende ndi kuzunza oyera mtima, iye anachita zimenezi asanadziwe choonadi chonena za Yesu Khristu. Mwanjira yomweyi, ife tikuyenera kuphunzitsa chidzitso choona cha Mulungu. kwa iwo amene sadziwa Mpingo wa Mulungu, Sabata, ndi Paska, kuma kuyakhula motsutsana nao. Pakutero tikhoza kuwatsogolera kukulandira dalitso la chipulumutso, zomwe limakondweretsa kwambiri.
Ndipo ananena nao, Mukani kudziko lonse lapansi, lalikirani Uthenga Wabwino kwa olengedwa onse. [16] Amene akhulupirira nabatizidwa, adzapulumutsidwa; koma amene sakhulupirira adzalangidwa. Marko 16:15–16
Mulungu Mpulumutsi wathu amene afuna anthu onse apulumuke, nafike pozindikira choonadi. 1 Timoteo 2:3–4
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi