Baibulo limachitira umboni za Mulungu Atate ndi Mulungu Amayi kudzera mwa Adamu ndi Heva.
Monga Heva amatchedwa “amayi wa amoyo onse,” anapereka moyo wakuthupi kwa anthu, ndipo Mulungu Amayi abwera padziko lapansi kudzapereka moyo wosatha kwa anthu.
Mulungu anati, “Tipange munthu m’chifanizo chathu, . . .” ndipo analenga mwamuna ndi mkazi, ndipo Iye anagwiritsa ntchito dzina lakuchulukitsa “Elohim” [milungu] koposa ka 2,500 m’ Baibulo.
Komanso, kuchitira umboni kuti Mulungu Amayi alipo, amene amapereka moyo wosatha kwa anthu kudzera mu chifuniro chawo cha kulenga zinthu zonse kuti zilandile moyo kokha kudzera mwa amayi.
Ndipo anati Mulungu, Tipange munthu m’chifanizo
chathu, monga mwa chikhalidwe chathu: . . .
Mulungu ndipo adalenga munthu m’chifanizo
chake, m’chifanizo cha Mulungu adamlenga iye;
adalenga iwo mwamuna ndi mkazi.
Genesis 1: 26–27
Ndipo mwamuna anamutcha dzina la mkazi wake,
Heva; chifukwa ndiye amake wa amoyo onse.
Genesis 3:20
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi