Iyi ndi filimu yayifupi kuchokera mu nkhani yowona.
Chaka chilichonse, mwana wamwamuna yemwe anali pa ntchito ya usilikali ankalandira
tchuti cha mphoto ndipo ankapita kwawo kwa mayi ake.
Msewu wopita kumudzi kwawo unali woipa, wopanda phula, ndiponso wodzala ndi miyala yotulukira kunja, zomwe zinachititsa kuti matayala a galimoto aphulike kangapo.
Mayiyo anapwanya miyalayo mosatopa, kaya kukugwa mvula kapena chipale chofewa kuti akonzere njira yoti mwana wake ayende bwino.
Panjira yomalizidwa ndi nsembe ndi chikondi cha amayi, mwana wake anakhetsa misozi yachiyamiko.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi