Chifukwa ndi kuikidwa m'manda ndi maliro a machimo a anthu,
ubatizo siutanthauza kusamba chabe,
koma ubatizo wokhala ndi tanthauzo la kumizidwa (kuikidwa m'manda)
ndicho choonadi cha m’Baibulo.
Popeza Baibulo limati, “Mphotho ya uchimo ndi imfa,”
anthu onse adzafa tsiku lina. Komabe, Mulungu amawalola
kuikiratu m’manda machimo awo kudzera mu ubatizo;
ndi kupereka moyo watsopano kwa amene abatizidwa,
monga Iye Anaukitsa Yesu kwa akufa.
Mulungu amapereka moyo wosatha kwa iwo
amene adya thupi la Yesu ndi kumwa mwazi Wake,
kuti asachimwenso
atachotsedwa machimo awo kudzera mu ubatizo.
Mulungu Amatipatsa
chikhululukiro cha Machimo
kudzera mu Ubatizo,
ndi Moyo Wosatha Kedzera mu
Paska ya Pangano Latsopano
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi