Pamene Abrahamu sanasiye ngakhale mwana Wake mmodzi yekha Isake, kumvera mawu a Mulungu, Mulungu anamdalitsa, nati mbeu zake zidzakhala zochuluka ngati nyenyezi zakumwamba. Masiku ano, nafenso, tidzalandira madalitso aakulu tikamamvera malamulo ndi malangizo a Mulungu.
Ngati tili ndi chikhulupiriro, sitimangosunga malamulo a Mulungu ndi chikhulupiriro chofunda,
koma kusintha kwina kumapezeka mwa ife.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi