Pangano latsopano ndi limene limapangitsa kuti anthu, amene Mulungu analenga, akhale ofunika kwambili.
Choonadi cha pangano latsopano ndicho chuma chakumwamba chimene ngakhale angelo akumwamba amalakalaka kusuzumilamo.
Mulungu wapereka choonadi ichi kwa anthu akumwamba okha amene adzalandira ufumu wakumwamba.
Iwo amene ali ndi thupi ndi magazi a Mulungu mwa kudya ndi kumwa mkate wa Paskha ndi vinyo, zimene Mulungu anati Anapangidwa mwa Mulungu, akhoza kukhala ana a Mulungu.
Atha kulandira chikhululukiro cha machimo ndi madalitso a moyo wosatha mu Ziyoni kumene Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi amakhala.
Taonani masiku adza, ati Yehova, ndipo ndidzapangana pangano latsopano ndi nyumba ya Israele, ndi nyumba ya Yuda; . . . ndidzaika chilamulo changa m'kati mwao, ndipo m'mtima mwao ndidzachilemba; ndipo ndidzakhala Mulungu wao, nadzakhala iwo anthu anga;
Yeremiya 31:31-33
Chifukwa chake Yesu anati kwa iwo, Indetu, indetu, ndinena ndi inu... Iye wakudya thupi langa ndi kumwa mwazi wanga ali nao moyo wosatha; ndipo Ine ndidzamuukitsa iye tsiku lomaliza.
Yohane 6:53-54
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi