Mamembala a Ziyoni amayamikiridwa chifukwa cha kupambana
kwawo kwapadera m’maphunziro awo, ntchito zodzipereka,
ndi moyo wachikhulupiriro, koma chofunika koposa
pakati pawo ndicho chikhulupiriro chawo mwa
Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi,
Zinsinsi za ufumu wakumwamba.
Zaka mazana ambiri pambuyo pa imfa
ya Mfumu Davide, mneneri Ezekieli analosera
kuti Mulungu adzabwera monga Davide ndi
pangano latsopano m’masiku otsiriza.
Khristu Ahnsahnghong, amene anabwera ngati Davide
wauzimu, anabwezeretsa Paska wa pangano latsopano
imene inathetsedwa mu AD 325, ndipo
anatidziwitsa kuti tingapulumutsidwe pokhapokha tikafika
kwa Mulungu Amayi, amene ali zenizeni
za pangano latsopano.
Davide mtumiki wanga adzakhala mtsogoleri
wao kosatha. Ndipo ndidzapangana nao pangano
la mtendere, lidzakhala pangano losatha nao, . . .
Ine ndidzakhala Mulungu wao, ndi iwo
adzakhala anthu anga.
Ezekieli 37:25-27
Taonani masiku adza, ati Yehova,
ndipo ndidzapangana pangano latsopano ndi
nyumba ya Israele, ndi nyumba ya Yuda; . . .
ndidzaika chilamulo changa m'kati mwao,
ndipo m'mtima mwao ndidzachilemba; ndipo
ndidzakhala Mulungu wao, nadzakhala iwo
anthu anga;
Yeremiya 31:31-33
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi