Anthu onse a dziko lapansi anaponyedwa pansi kuchokera kumwamba chifukwa chochita tchimo lalikulu limene limatsogolera ku imfa. Choncho, tiyenera kukumbukira nthawi zonse kuti ndife ochimwa, tipewe kunyada, kukana kufanana ndi dziko loipali, ndikukhala ndi moyo wa kulapa kuti tipulumutsidwe pa chiweruzo chimene chidzabwere pambuyo pa imfa yathu yakuthupi.
Amene alapa moona mtima amaperekanso mitima yawo kutsogolera ena ku kulapa. Monga mmene mayi weniweni ndi mayi wabodza anavumbulutsidwira kudzera mu zochita zawo pachiweruzo cha Solomoni, amenenso afika pa kulapa kumene kumatsogolera ku chipulumutso amavumbulutsanso mitima yawo kudzera mu zochita zawo.
Sindinadza Ine kuitana olungama, koma ochimwa kuti atembenuke mtima. Luka 5:32
Ndinena kwa inu, Iaitu; koma ngati simutembenuka mtima, mudzaonongeka nonse chimodzimodzi. Luka 13:5
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi