Anthu a Mpingo wa Mulungu amakhulupirira kuti Khristu Ahnsahnghong
ndi Khristu Wobwera Kachiwiri chifukwa Iye ndiye yekhayo amene walola
anthu, amene anaikidwa kuifa chifukwa cha tchimo la kudya kuchokera ku Mtengo
Wodziwitsa Zabwino ndi Zoipa, kuti adyenso ku Mtengo wa Moyo
ndipo analonjeza moyo wosatha kudzera mu Paska wa pangano latsopano
lomwe ndi zenizeni za Mtengo wa Moyo.
Monga Ayuda anazunza Yesu zaka 2,000 zapitazo, za Iye monga mwana wa mmisiri wamatabwa, lmasiku anonso, anthu ambiri sakhulupirira Khristu Ahnsahnghong amene anabwera kudzapereka chipulumutso.
Komabe, amene akupulumutsidwa akuzindikira pangano latsopano Paska kuti ndi zenizeni za Mtengo wa Moyo ndi kubwera kwa Iye.
Ndipo m’phiri limeneli Yehova wa makamu adzakonzera . . . phwando la vinyo wa pamitsokwe, . . .
Iye wameza imfa kunthawi yonse; ndipo Ambuye Mulungu adzapukuta misozi pa nkhope zonse; ndipo chitonzo cha anthu ake adzachichotsa padziko lonse lapansi; chifukwa Yehova wanena.
Ndipo adzanena tsiku limenelo, Taonani, uyu ndiye Mulungu wathu; . . .
Yesaya 25:6–9
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi