Anthu zikwi zana limodzi mphambu zikwi makumi awiri ku Nineve,
amene sanathe kusiyanitsa kumanja ndi kumanzere,
pamene Yona analalikira kwa iwo mwa kumvera lamulo la Mulungu,
onse analapa. Mu m'badwo uno, nawonso,
tiyenera kulalikira Paskha wa Chipangano Chatsopano choonadi
cha chipulumutso ndi chikhululukiro cha machimo kwa anthu
onse amene sakumvetsetsa malamulo a Mulungu.
Monga omwe anaika mwazi wa nkhosa ya Paskha pa zitseko
iwo anapulumutsidwa ku mliri mu nthawi ya Mose,
anthu odya thupi ndi mwazi wa Kristu kupyolera
mu mkate ndi vinyo wa Paskha akhoza kulandira
chizindikiro cha chipulumutso
mu Chipangano chatsopano.
Khristu Ahnsahnghong anachitira umboni wa Paskha pangano latsopano.
Ndi Mulungu amene wadza kudzatikhululukira machimo athu
m'masiku ano otsiriza, monga mwa maulosi a m'Baibulo.
Taonani masiku adza, ati Yehova,
ndipo ndidzapangana pangano latsopano
ndi nyumba ya Israele, ndi nyumba ya Yuda . . .
ndidzakhululukira mphulupulu yao,
ndipo sindidzakumbukira tchimo lao. Yeremiya 31:31–34
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi