Mulungu, amene akuona mapeto kuchokera kuchiyambi, anatichenjeza mwamphamvu kusawonjezera kapena kusachotsera chilichonse pa mawu a m'Baibulo.
Baibulo limatiphunzitsa kuti tisunge malamulo a Mulungu monga tsiku la sabata ndi Paskha,
komanso limatiphunzitsanso, Akristu, kukhala ndi moyo monga mchere ndi kuunika kwa dziko lapansi.
Monga m’mene Mulungu anatsogolera ana a Isiraeli m'dziko la Kanani ndipo anawadalitsa, mu m'badwo uno nawonso, tikamalekeza Mulungu m'mabanja athu, kuntchito kwathu, ndi anansi athu, malinga ndi zomwe Mulungu Ahnsahnghong ndi Amayi akumwamba, tidzavomerezedwa kukhala m’moyo wathu ngati Akhristu ndi kulandira mdalitso wolowa Ufumu wa Kumwamba.
Chomwecho muwalitse inu kuunika kwanu
pamaso pa anthu, kuti pakuona ntchito
zanu zabwino, alemekeze Atate wanu wa Kumwamba. Mateyu 5:16
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi