Yesu anasonyeza momvekera bwino kuti munthu ali ndi thupi ndi mzimu kupyolera mu fanizo la “Munthu wachuma ndi Lazaro,” ndipo anatiphunzitsa ife kulingalira za kumwamba ndi gehena kumene mzimu wathu uliwonse udzatumizidwako pambuyo pa imfa ya matupi athu akuthupi.
Tsiku lililonse, mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhala ngati Akhristu oyera ndi aumulungu, kusiya chikhalidwe chawo chonse chauchimo mogwirizana ndi mawu a Mulungu pakuti munthu aliyense adzaweruzidwa molingana ndi zomwe wachita, ndi chiphunzitso cha Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai amene anati, "Ndikofunika kukhala ndi moyo wa kumvera ndi kulapa molingana ndi ziphunzitso za Mulungu."
Ndipo ndinaona akufa, aakulu ndi aang'ono alinkuima kumpando wachifumu; ndipo mabuku anatsegulidwa; ndipo buku lina linatsegulidwa, ndilo la moyo; ndipo akufa anaweruzidwa mwa zolembedwa m'mabuku, monga mwa ntchito zao. Chivumbulutso 20:12
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi