Mulungu anabwera m'thupi kachiwiri pa tsiku lozizira mu 1918, molingana ndi maulosi a m’Baibulo. Anagwira ntchito yamiyara ndi kulalikira choonadi cha pangano latsopano m'moyo wovuta, koma anthu anamunyoza, ponena kuti sanali Mulungu.
Komabe, njira yomuzindikira Iye, amene ndi chinsinsi cha Mulungu, si nzeru za anthu koma m'Baibulo. khristu Ahnsahnghong anatipatsa moyo wosatha ndi vinyo wa Paska wa pangano latsopano; Iye ndi Mulungu wathu ndi khristu amene anabweranso chifukwa cha chipulumutso chathu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi