Monga kwalembedwa, “Adzaoneka kachiwiri kubweretsa chipulumutso kwa iwo amene akumuyembekezera,” Khristu Ahnsahnghong anabwera ku dziko lino lapansi, ndipo Iye anatiphunzitsa za Paska wa pangano latsopano amene anthu adamutaya, anakwaniritsa maulosi onse a Mfumu Davide, ndipo anaulula za Amayi Yerusalemu Wakumwamba. Chifukwa cha izi, mamembala a Mpingo wa Mulungu lero akhoza kukhala ndi chiyembekezo cha ufumu wa kumwamba ku Ziyoni.
Ndipo popeza kwaikikatu kwa anthu kufa kamodzi, ndipo atafa,
chiweruziro;kotero Khristunso ataperekedwa nsembe kamodzi
kukasenza machimo a ambiri, adzaonekera pa nthawi yachiwiri,
wopanda uchimo, kwa iwo amene amlindirira,
kufikira chipulumutso.
Ahebri 9: 27-28
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi