Monga momwe oyera mtima a Mpingo woyamba ankaonera kulalikira
pakati pa kuzunzidwa ngati chimwemwe, ngati tizindikira chikondi ndi kudzipereka
kwa Khristu amene adachita chotetezera machimo a anthu,
tidzakhala othokoza ngakhale pazowawa
zomwe timakumana nazo m’moyo wathu wachikhulupiriro.
Khristu Ahnsahnghong ndi Amayi a Kumwamba anabwera kudzapulumutsa ochimwa kuimfa.
Oyera mtima a Mpingo wa Mulungu akulalikira uthenga wabwino ndi mtima wawo wonse ndi nzeru zawo,
poyembekeza kuti anthu azindikira chisomo cha Mulungu
kuti alape kwathunthu.
koma popeza mulawana ndi Khristu zowawa zake, kondwerani: kutinso pa vumbulutso la ulemerero wake mukakondwere kwakukulukulu. 1 Petro 4:13
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi