Mu nthawi ya Chipangano Chakale, Mulungu Yehova anapatsa Aisraele mana, ndipo monga momwe kwalembedwera mu Chivumbulutso 2, “Kwa iye wolakika, ndidzampatsa mana obisika,” lero, Khristu Ahnsahnghong amapereka mana obisika kudzera mu mkate ndi vinyo wa Paska mu Mpingo wa Mulungu. Iye ndiye Mulungu amene wapatsa anthu moyo wosatha.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi