Mosiyana ndi ansembe a Chipangano Chakale, Melkizedeki anadalitsa Abrahamu ndi mkate komanso vinyo. Chomwechonso, potsatira dongosolo la Melkizedeki, Khristu Yesu Wobwera Koyamba ndi Khristu Wobwera Kachiwiri Ahnsahnghong apatsa anthu madalitso a chikhululukiro cha machimmo ndi moyo wosatha kudzera mu mkate ndi vinyo wa Paska. Ichi nchifukwa chake mamembala a Mpingo wa Mulungu padziko lonse amasunga Paska masiku ano.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi