Aneneri amene analemba Baibulo ankakhala m ‘nthawi zosiyana ndipo anali ndi ntchito zosiyana ndi umunthu wosiyana, komabe anuziridwa ndi Mzimu Woyera wa Mulungu, anasiya maulosi osasinthasintha, kutionetsa za “chifukwa chake anthu anabwera ku dziko lapansi ndi kumene tikupita.”
Popeza kuti Baibulo ndi loona, tiyenera kukhulupirira maulosi onena za Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
Bukhu la Yesaya linaneneratu za kuzunzika kwa Yesu zaka 700 asanabwere, ndipo buku la Yobu linalemba za kayendedwe ka madzi ndi mfundo yakuti dziko lapansi linalenjekedwa m’mlengalenga zaka 3,500 zapitazo, mfundo zimene sayansi inangotulukira m’zaka za m’ma 17centur.
Lemba lililonse adaliuzira Mulungu, ndipo
lipindulitsa pa chiphunzitso, chitsutsano,
chikonzero, chilangizo cha m’chilungamo:
kuti munthu wa Mulungu akhale woyenera,
wokonzeka kuchita ntchito iliyonse yabwino.
2 Timoteo 3:16–17
“Ayala kumpoto popanda kanthu,
nalenjeka dziko pachabe.”
Yobu 26:7
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi