Mulungu ali ndi mphamvu yolamulira mwayi ndi tsoka la anthu onse, moyo ndi imfa, ndi kumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo. Ngati ife tidalira mphamvu za dziko, chuma, ndi chidziwitso, m’malo mwa Mulungu monga mphamvu yathu, tidzawonongedwa monga mfumu ya ku Samariya inafa pokudalira mulungu wachikunja pamene iye anavulala.
monga momwe makolo a chikhulupiriro monga Davide, Habakuku, ndi Zekariya anagonjetsa zopinga poona Mulungu ngati mphamvu zawo ndipo nthawi zonse amadalira Mulungu muzochitika zonse, mamembala a Mpingo wa Mulungu amakhala ndi moyo wachimwemwe ndi wosangalala wa chikhulupiriro, akuyenda m’njiraewu yopambana ya uthenga wabwino podalira Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi.
(K)oma ndidzakondwera mwa Yehova, ndidzasekerera mwa Mulungu wa chipulumutso changa.
Yehova, Ambuye, ndiye mphamvu yanga, asanduliza mapazi anga ngati a mbawala, nadzandipondetsa pa misanje yanga.
Habakuku 3:18–19
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi