Mfundo yakuti Mulungu sanatumize mngelo
m 'malo mwake, koma anabwera padziko lapansi
pano kuti akhale nsembe ndi kupirira mavuto
onse ndi zowawa zomwe tinayenera kudutsa,
zikuwonetsa bwino momwe Mulungu
amasangalalira ndi kukonda anthu.
Ziyoni ndi malo amene kuyamika
ndi chiyembekezo cha kumwamba
zimasefukira mu pangano latsopano.
Popeza Atate Ahnsahnghong ndi Mulungu
Amayi, pamodzi ndi abale ndi alongo, ali
pamodzi ku Ziyoni, mamembala a Mpingo
wa Mulungu amagonjetsa nkhawa
zodandaulitsa ndi nkhawa za
dziko lapansi ndi chimwemwe.
Okondedwa, tikondane wina ndi mnzake:
chifukwa kuti chikondi chichokera kwa
Mulungu, ndipo yense amene akonda,
abadwa kuchokera kwa Mulungu,
namzindikira Mulungu.
Iye wosakonda sazindikira Mulungu;
chifukwa Mulungu ndiye chikondi.
[1 Yohane 4:7–8]
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi