Mulungu anakonzeratu zimene zidzachitike asanalenge chilengedwe
ndipo wakhala akugwira ntchito yamaomboledwe mogwirizana ndi maulosi a m’Baibulo.
Choncho, tiyenera kukhulupirira maulosi.
Njira yopulumutsira ndi kutetezedwa ku matsoka mu m’badwo uno ndi kudzera mu chizindikiro cha Mulungu, Paskha.
Dziko lonse lapansi likukhamukira ku Mpingo wa Mulungu umene umasunga Paskha wa pangano latsopano.
Tiyenera kudziwa kuti zonse zikukwaniritsidwa motsatira maulosi a Mulungu.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi