Pamene Yesu ananena kuti, “Ndinalakalaka ndithu kudya Paska uwu,” ndipo anatumiza Petro ndi Yohane kukakonzekera, cholinga Chake chinali kupatsa anthu moyo wosatha ndi chipulumutso kudzera mu Paska. Kudzera mu Paska wa pangano latsopano, amene mamembala a Mpingo wa Mulungu amasunga mopatulika potsatira chitsanzo cha Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amai, lonjezo la moyo wosatha laperekedwa.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi