Zinthu zonse za m 'dzikoli zinalengedwa mwa chifuniro cha Mulungu. Mulungu analenga zamoyo zonse kuti zilandire moyo kudzera mwa amai. Ichi ndi chifuniro chachikulu cha Mulungu kuti adziwitse za kukhalapo kwa Amai a Kumwamba, amene amapereka moyo wosatha kwa anthu.
Amai Akumwamba amene Baibulo limawachitira umboni za munthu analengedwa m'chifanizo cha Mulungu Atate amene ali ndi chifanizo cha mwamuna, ndipo mkazi analengedwa m' chifanizo cha Mulungu Amayi amene ali ndi chifanizo cha mkazi.
Monga anthu atchula chifaniziro chachimuna cha Mulungu "Atate" kwa zaka masauzande ambiri, tiyenera kuzindikira Mulungu Amayi amene Baibulo limachitira umboni za iye ndi kumulandira. Umenewu ndi nzeru imene imatitsogolera kumwamba.
Koma Yerusalemu wa kumwamba uli waufulu, ndiwo amai wathu. . . . sitili ana a mdzakazi, komatu a mfulu. Agalatiya 4:26-31
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi