Utatu wa Mulungu umatanthauza kuti Mulungu mmodzi Atate amagwiritsa ntchito dzina losiyana mu M’badwo wa Atate, mu M’badwo wa Mwana, ndi mu M’badwo wa Mzimu Woyera kutsogolera anthu ku Ufumu wosatha wa Kumwamba.
Popeza kuti Mpingo wa Mulungu umakhulupirira kuti Mulungu Atate Yehova, Mulungu Mwana Yesu, ndi Mulungu Mzimu Woyera Ahnsahnghong ndi Mulungu mmodzi, mamembala a mpingo amapemphera m’dzina la Khristu Ahnsahnghong, akulalikira ulemerero Wake.
“Ine ndi Atate ndife amodzi.”
Yohane 10:30
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi