M’Baibulo monse, pali ziphunzitso zambiri zokhudza kulemekeza makolo.
Pakati pa izi, Mulungu adakondwera ndi zochita za Rute za kudzipereka kwa Naomi ndipo adazilemba M’malemba ngati chitsanzo cha umulungu chomwe chimakhala chitsanzo kwa ana akumwamba.
Mamembala a Mpingo wa Mulungu, m’malo motengera chikondi chozirara cha nthawi ino, iwo amatsatira ziphunzitso za Khristu Ahnsahnghong ndi Mulungu Amayi, pochita m’chitidwe olemekeza makolo.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi