Kumwamba ndi kwawo kwa aliyense amene anabadwa ndi kukhala padziko lapansi. Choncho, Mulungu anatiphunzitsa kuganizira za dziko limene tinachokamo.
Malingana ndi ziphunzitso za Khristu Ahnsahnghong ndi Amai Akumwamba, mamembala a Mpingo wa Mulungu azindikira kuti anthu anatsikira padziko lapansi chifukwa cha machimo amene anachita kumwamba. Iwo akuyesetsa kukhala ndi moyo wopindulitsa ndi woyenera.
119 Bundang P.O.Box, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Rep. of KOREA
Tel 031-738-5999 Fax 031-738-5998
Likulu la Ofesi: 50, Sunae-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
Mpingo Waukulu: 35, Pangyoyeok-ro, Bundang-gu, Seongnam-si, Gyeonggi-do, Dziko la Korea
ⓒ Gulu la Utumiki wa Dziko Lonse la Mpingo wa Mulungu. Ma Umwini onse ndi Otetezedwa Mfundo za Zinsinsi